-
1 Akorinto 7:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Amene amagwiritsira ntchito dzikoli azikhala ngati amene sakuligwiritsira ntchito mokwanira, chifukwa zochitika zapadzikoli zikusintha.
-
-
Tito 2:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mulungu waonetsa kukoma mtima kwake kwakukulu kumene kumabweretsa chipulumutso kwa anthu, kaya akhale otani.+ 12 Zimenezi zimatiphunzitsa kukana moyo wosaopa Mulungu. Zimatiphunzitsanso kuti tisamalakelake zinthu zoipa zamʼdzikoli,+ koma kuti tikhale oganiza bwino, achilungamo ndi odzipereka kwa Mulungu mʼdzikoli*+
-