Machitidwe 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti si zololeka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa mtundu wina kapena kumuyandikira.+ Koma Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti wodetsedwa kapena wonyansa.+
28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti si zololeka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa mtundu wina kapena kumuyandikira.+ Koma Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti wodetsedwa kapena wonyansa.+