Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika.
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika.