Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:28 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 290-291 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 30-31 Nsanja ya Olonda,12/1/1990, tsa. 8
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika.