-
Luka 2:34, 35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Komanso Simiyoni anadalitsa makolowo ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamvera! Mwanayu waikidwa kuti ambiri agwe+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli.+ Komanso kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+ 35 (inde, lupanga lalitali lidzakubaya)+ kuti zimene anthu ambiri akuganiza mumtima mwawo zionekere poyera.”
-