Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu a mʼnyumba ya Davide ndiponso a ku Yerusalemu ndidzawapatsa mzimu wanga posonyeza kuti ndawakomera mtima ndipo udzawalimbikitsa kundipempha mochonderera. Iwo adzayangʼana kwa munthu amene anamubaya,+ ndipo adzamulirira ngati mmene angachitire polirira mwana yekhayo wamwamuna. Adzamulira kwambiri ngati akulira maliro a mwana wamwamuna woyamba kubadwa.

  • Chivumbulutso 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena