Yohane 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala. Yohane 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndabwera monga kuwala mʼdziko,+ kuti aliyense wokhulupirira ine asapitirize kukhala mumdima.+ 1 Yohane 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komatu ngati tikuyenda mʼkuwala mofanana ndi mmenenso iye alili mʼkuwala, ndiye kuti ndife ogwirizana ndipo magazi a Yesu, yemwe ndi Mwana wake, akutiyeretsa ku machimo onse.+
36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala.
7 Komatu ngati tikuyenda mʼkuwala mofanana ndi mmenenso iye alili mʼkuwala, ndiye kuti ndife ogwirizana ndipo magazi a Yesu, yemwe ndi Mwana wake, akutiyeretsa ku machimo onse.+