Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamene ophunzira a Yohane ankabwerera, Yesu anayamba kuuza gulu la anthu za Yohane kuti: “Kodi munapita mʼchipululu kukaona chiyani?+ Kodi munapita kukaona bango logwedezeka ndi mphepo?+

  • Mateyu 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Malemba amanena za iyeyu kuti: ‘Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga kuti atsogole kukakukonzera njira!’+

  • Luka 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiye mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya chifukwa pemphero lako lopembedzera lamveka ndithu. Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamupatse dzina lakuti Yohane.+

  • Luka 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Komanso adzatsogola monga kalambulabwalo wa Mulungu ali ndi mzimu ndi mphamvu ngati za Eliya.+ Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana+ ndipo anthu osamvera adzawatembenuzira ku nzeru yeniyeni ya anthu olungama. Adzachita zimenezi kuti asonkhanitse anthu amene akonzekera kutumikira Yehova.”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena