Yohane 11:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Zitatero ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanitsa Khoti Lalikulu la Ayuda* nʼkunena kuti: “Kodi tichite chiyani pamenepa? Chifukwatu munthu uyu akuchita zizindikiro zochuluka.+
47 Zitatero ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanitsa Khoti Lalikulu la Ayuda* nʼkunena kuti: “Kodi tichite chiyani pamenepa? Chifukwatu munthu uyu akuchita zizindikiro zochuluka.+