Yohane 11:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Zitatero ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanitsa Khoti Lalikulu la Ayuda*+ ndi kunena kuti: “Kodi tichite chiyani pamenepa, chifukwa munthu uyu akuchita zizindikiro zochuluka?+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:47 Yesu—Ndi Njira, tsa. 215 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, ptsa. 11-125/15/1989, ptsa. 8-9
47 Zitatero ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanitsa Khoti Lalikulu la Ayuda*+ ndi kunena kuti: “Kodi tichite chiyani pamenepa, chifukwa munthu uyu akuchita zizindikiro zochuluka?+