Machitidwe 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzidzidzi, kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo phokoso lake linadzaza mʼnyumba yonse imene iwo anali.+ Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+
2 Mwadzidzidzi, kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo phokoso lake linadzaza mʼnyumba yonse imene iwo anali.+
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+