Machitidwe 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamaliza kupemphera mochonderera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka. Kenako onse anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+
31 Atamaliza kupemphera mochonderera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka. Kenako onse anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+