-
Machitidwe 1:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho nʼkofunika kuti alowedwe mʼmalo ndi mmodzi mwa anthu amene ankayenda nafe pa nthawi yonse imene Ambuye Yesu ankachita zinthu zosiyanasiyana pakati pathu. 22 Munthu wake akhale amene ankayenda nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa ndi Yohane,+ kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Munthu ameneyu akhale mboni ya kuuka kwa Yesu pamodzi ndi ife.”+
-