-
Maliko 14:70Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
70 Apanso Petulo anakana. Patapita kanthawi pangʼono, amene anali ataimirira chapafupi anayambanso kuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli mʼgulu la ophunzira ake. Ndipo ndiwenso Mgalileya.”
-
-
Machitidwe 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Azibambowo anawafunsa kuti: “Amuna inu a ku Galileya, nʼchifukwa chiyani mwangoima nʼkumayangʼana kumwamba? Yesu, amene watengedwa pakati panu kupita kumwambayu, adzabwera mʼnjira yofanana ndi mmene mwamuonera akupita kumwamba.”
-