Machitidwe 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Usiku womwewo, anawatenga nʼkuwatsuka mabala awo. Pasanapite nthawi yaitali, iye ndi anthu onse a mʼbanja lake anabatizidwa.+ Machitidwe 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.
33 Usiku womwewo, anawatenga nʼkuwatsuka mabala awo. Pasanapite nthawi yaitali, iye ndi anthu onse a mʼbanja lake anabatizidwa.+
8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.