Machitidwe 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene ankalengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu+ ndiponso wonena za dzina la Yesu Khristu, ankabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+
12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene ankalengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu+ ndiponso wonena za dzina la Yesu Khristu, ankabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+