Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzidya mkate wopanda zofufumitsa kwa masiku 7.+ Pa tsiku loyamba muzichotsa mʼnyumba zanu ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa chifukwa aliyense wodya mkate wokhala ndi zofufumitsa, kuchokera pa tsiku loyamba kukafika pa tsiku la 7, munthu wochita zimenezi aziphedwa kuti asakhalenso mu Isiraeli.

  • Ekisodo 23:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzichita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda zofufumitsa masiku 7 pa nthawi imene inaikidwa mʼmwezi wa Abibu*+ mogwirizana ndi zimene ndinakulamulani, chifukwa munatuluka mu Iguputo mʼmwezi umenewu. Ndipo palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena