1 Akorinto 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndine wamngʼono kwambiri pa atumwi onse ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza mpingo wa Mulungu.+ 1 Atesalonika 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso sitinkafuna ulemerero wochokera kwa anthu, kaya kuchokera kwa inu kapena kwa anthu ena, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu+ tikanatha kupempha kuti mutilipirire zinthu zina kuti mutithandize.
9 Ineyo ndine wamngʼono kwambiri pa atumwi onse ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza mpingo wa Mulungu.+
6 Komanso sitinkafuna ulemerero wochokera kwa anthu, kaya kuchokera kwa inu kapena kwa anthu ena, ngakhale kuti monga atumwi a Khristu+ tikanatha kupempha kuti mutilipirire zinthu zina kuti mutithandize.