Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma pamene ndinasowa zofunika zina ndili kwanuko, sindinalemetse munthu aliyense, popeza abale amene anachokera ku Makedoniya anandipatsa zonse zimene ndinkafunikira.+ Ndithu, ndinayesetsa kuti ndisakulemetseni mʼnjira iliyonse, ndipo ndipitirizabe kutero.+

  • 2 Atesalonika 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.*+ Mʼmalomwake, tinagwira ntchito mwakhama komanso ndi mphamvu zathu zonse usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+

  • 2 Atesalonika 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipotu pamene tinali ndi inu, tinkakupatsani lamulo lakuti: “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena