1 Atesalonika 4:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muziyesetsa kukhala mwamtendere,+ musamalowerere nkhani za ena+ ndipo muzigwira ntchito ndi manja anu+ mogwirizana ndi malangizo amene tinakupatsani. 12 Muzichita zimenezi kuti mukhale ndi makhalidwe amene angachititse kuti anthu akunja azikulemekezani+ ndiponso kuti mukhale osasowa kanthu. 1 Timoteyo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira, makamaka a mʼbanja lake, wakana chikhulupiriro ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.+
11 Muziyesetsa kukhala mwamtendere,+ musamalowerere nkhani za ena+ ndipo muzigwira ntchito ndi manja anu+ mogwirizana ndi malangizo amene tinakupatsani. 12 Muzichita zimenezi kuti mukhale ndi makhalidwe amene angachititse kuti anthu akunja azikulemekezani+ ndiponso kuti mukhale osasowa kanthu.
8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira, makamaka a mʼbanja lake, wakana chikhulupiriro ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.+