Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamabwezere choipa pa choipa.+ Muziganizira zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.