1 Atesalonika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onetsetsani kuti pasapezeke wobwezera choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse muziyesetsa kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo. 1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni.
15 Onetsetsani kuti pasapezeke wobwezera choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse muziyesetsa kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+
23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo.
9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni.