1 Atesalonika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+ 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 28
15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+