2 Atesalonika 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+ 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, tsa. 5
8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+