Machitidwe 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene ankalengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu+ ndiponso wonena za dzina la Yesu Khristu, ankabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+ Machitidwe 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.
12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene ankalengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu+ ndiponso wonena za dzina la Yesu Khristu, ankabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+
8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.