-
Machitidwe 17:30, 31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Nʼzoona kuti Mulungu analekerera nthawi yomwe anthu sankadziwa zinthu,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape. 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+
-