Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa ku Chilamulo chimene chinkatimanga, kuti tikhale akapolo mʼnjira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati mʼnjira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+

  • Agalatiya 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Komanso ngati mukutsogoleredwa ndi mzimu, simuli pansi pa chilamulo.

  • Akolose 2:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuwonjezera pamenepo, ngakhale kuti munali akufa chifukwa cha machimo anu komanso chifukwa choti munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu.+ Mokoma mtima anatikhululukira machimo athu onse+ 14 ndipo anafafaniza Chilamulo+ chimene chinali ndi malamulo ambirimbiri+ omwe ankatitsutsa.+ Iye anachichotsa pochikhomerera pamtengo wozunzikirapo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena