Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira, anawapatsa mphamvu kuti akhale ana a Mulungu,+ chifukwa choti ankakhulupirira dzina lake.+ Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+
12 Komabe onse amene anamulandira, anawapatsa mphamvu kuti akhale ana a Mulungu,+ chifukwa choti ankakhulupirira dzina lake.+
5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+