-
2 Akorinto 5:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Tikudziwa kuti nyumba yathu yapadziko lapansi pano kapena kuti tenti ino, ikadzaphwasuka,+ tidzalandira nyumba yochokera kwa Mulungu. Imeneyo idzakhala nyumba yosamangidwa ndi manja,+ koma yamuyaya ndipo idzakhala kumwamba. 2 Chifukwa mʼnyumba imene tikukhalayi tikubuula ndipo tikufunitsitsa kuvala nyumba yathu yakumwamba,+
-