2 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tikudziwa kuti nyumba yathu ya padziko lapansi pano,+ msasa uno,+ ikadzaphwasuka,+ tidzalandira nyumba yochokera kwa Mulungu. Imeneyo idzakhala nyumba yosamangidwa ndi manja,+ koma yamuyaya,+ ndipo idzakhala kumwamba. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, tsa. 153/1/1995, tsa. 30
5 Tikudziwa kuti nyumba yathu ya padziko lapansi pano,+ msasa uno,+ ikadzaphwasuka,+ tidzalandira nyumba yochokera kwa Mulungu. Imeneyo idzakhala nyumba yosamangidwa ndi manja,+ koma yamuyaya,+ ndipo idzakhala kumwamba.