Yohane 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+ Aroma 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pofa imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana naye.+ 1 Akorinto 15:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Monga zilili kuti panopa tikufanana ndi wopangidwa ndi dothi uja,+ tidzafanananso ndi wakumwambayo.+
15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+
5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pofa imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana naye.+
49 Monga zilili kuti panopa tikufanana ndi wopangidwa ndi dothi uja,+ tidzafanananso ndi wakumwambayo.+