Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 28:30, 31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Choncho Paulo anakhalabe kwa zaka ziwiri zathunthu mʼnyumba yomwe ankapanga lendi,+ ndipo anthu onse omwe ankabwera kudzamuona ankawalandira ndi manja awiri. 31 Ankawalalikira za Ufumu wa Mulungu komanso kuwaphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu, ndi ufulu wonse wa kulankhula*+ popanda choletsa.

  • Akolose 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma mukuyenera kupitiriza kukhala mogwirizana ndi chikhulupiriro chanu,+ muli okhazikika pamaziko,+ muli olimba+ komanso muli osasunthika pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva, umenenso unalalikidwa padziko lonse.*+ Ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wa uthenga wabwino umenewu.+

  • 2 Timoteyo 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma iwe ukhalebe woganiza bwino pa zinthu zonse, uzipirira mavuto,+ uzigwira ntchito ya mlaliki* ndiponso uzikwaniritsa mbali zonse za utumiki wako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena