Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+ Aroma 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe sizikutanthauza kuti mawu a Mulungu sanakwaniritsidwe. Chifukwa si onse omwe ndi mbadwa za Aisiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+ Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+
29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+
6 Komabe sizikutanthauza kuti mawu a Mulungu sanakwaniritsidwe. Chifukwa si onse omwe ndi mbadwa za Aisiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+
29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+