2 Timoteyo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lalikira mawu.+ Uzilalikira modzipereka, pa nthawi yabwino ndi pa nthawi yovuta. Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira, ndipo uzichita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa+ ndiponso moleza mtima kwambiri.
2 Lalikira mawu.+ Uzilalikira modzipereka, pa nthawi yabwino ndi pa nthawi yovuta. Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira, ndipo uzichita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa+ ndiponso moleza mtima kwambiri.