Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uziwadzudzula+ pamaso pa onse kuti ena onsewo akhale ndi mantha.*

  • Tito 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.

  • Tito 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Akhalenso wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi mfundo zolondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.

  • Tito 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Umboni umenewu ndi woona. Chifukwa cha zimenezi, pitiriza kuwadzudzula mwamphamvu kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba.

  • Tito 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu pogwiritsa ntchito ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Usalole kuti munthu aliyense akuderere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena