Tito 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu mogwirizana ndi ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Munthu aliyense asakuderere.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, tsa. 24
15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu mogwirizana ndi ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Munthu aliyense asakuderere.+