Akolose 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma kuwonjezera pa zonsezi, valani chikondi,+ chifukwa chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu kwambiri kuposa chinthu china chilichonse.+ 1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Cholinga cha malangizo amenewa nʼchakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera, mʼchikumbumtima chabwino ndiponso mʼchikhulupiriro+ chopanda chinyengo. 1 Yohane 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale okondedwa, ngati Mulungu anatikonda chonchi, ndiye kuti ifenso tikuyenera kumakondana.+
14 Koma kuwonjezera pa zonsezi, valani chikondi,+ chifukwa chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu kwambiri kuposa chinthu china chilichonse.+
5 Cholinga cha malangizo amenewa nʼchakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera, mʼchikumbumtima chabwino ndiponso mʼchikhulupiriro+ chopanda chinyengo.