Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+ Salimo 147:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yakobo amamuuza mawu ake,Ndipo Isiraeli amamuuza malangizo ake komanso zigamulo zake.+ 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+ Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+
19 Yakobo amamuuza mawu ake,Ndipo Isiraeli amamuuza malangizo ake komanso zigamulo zake.+ 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+
38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+