Aroma 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse amene anachimwa asakudziwa Chilamulo, adzafa asakudziwa Chilamulo.+ Koma onse amene anachimwa akudziwa Chilamulo, adzaweruzidwa mogwirizana ndi Chilamulocho.+ Aroma 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+ Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+
12 Anthu onse amene anachimwa asakudziwa Chilamulo, adzafa asakudziwa Chilamulo.+ Koma onse amene anachimwa akudziwa Chilamulo, adzaweruzidwa mogwirizana ndi Chilamulocho.+
13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+
10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+