-
Yohane 17:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Sindikupempherera awa okha, koma ndikupemphereranso amene amakhulupirira ine atamvetsera zimene iwo amaphunzitsa. 21 Ndikuchita zimenezi kuti onsewa akhale amodzi+ ngati mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife nʼcholinga choti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.
-