1 Petulo 3:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+ 2 koma chifukwa choti aona khalidwe lanu labwino*+ komanso ulemu wanu waukulu.
3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+ 2 koma chifukwa choti aona khalidwe lanu labwino*+ komanso ulemu wanu waukulu.