1 Akorinto 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mkaziwe, ukudziwa bwanji, mwina ukakhalabe ndi mwamuna wako ungamʼpulumutse?+ Kapena mwamunawe, ukudziwa bwanji, mwina ukakhalabe ndi mkazi wako ungamʼpulumutse?
16 Mkaziwe, ukudziwa bwanji, mwina ukakhalabe ndi mwamuna wako ungamʼpulumutse?+ Kapena mwamunawe, ukudziwa bwanji, mwina ukakhalabe ndi mkazi wako ungamʼpulumutse?