Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mukakakhala ndi ana komanso zidzukulu ndipo mukakakhala nthawi yaitali mʼdzikomo, nʼkuchita zinthu zokuwonongetsani popanga chifaniziro chosema+ cha chinthu chilichonse, nʼkuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, moti nʼkumukhumudwitsa,+ 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafa mwamsanga mʼdziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzakhala mʼdzikomo kwa nthawi yaitali chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+

  • 2 Akorinto 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Choncho chokani pakati pawo ndipo musiyane nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+

  • 1 Yohane 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ana anga okondedwa, muzipewa mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena