-
Agalatiya 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndinapita kumeneko chifukwa ndinauzidwa mʼmasomphenya kuti ndipiteko. Ndipo abale ndinawafotokozera uthenga wabwino umene ndikuulalikira kwa anthu a mitundu ina. Koma ndinachita zimenezi mwachinsinsi kwa abale odalirika okha pofuna kutsimikizira kuti utumiki wanga sukupita pachabe.
-