Machitidwe 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pa mavuto amene anakumana nawo, iye anaonekera wamoyo kwa atumwiwo pogwiritsa ntchito maumboni ambiri otsimikizirika.+ Iwo anamuona masiku onse 40 ndipo ankawauza za Ufumu wa Mulungu.+ Machitidwe 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho atasonkhana, anamufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu kwa Aisiraeli panopa?”+
3 Pambuyo pa mavuto amene anakumana nawo, iye anaonekera wamoyo kwa atumwiwo pogwiritsa ntchito maumboni ambiri otsimikizirika.+ Iwo anamuona masiku onse 40 ndipo ankawauza za Ufumu wa Mulungu.+