10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti mʼdzina la Yesu Khristu wa ku Nazareti uja,+ amene inu munamuphera pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa,+ kudzera mwa iyeyo munthuyu waima patsogolo panu ali bwinobwino.
30 Koma Mulungu anamuukitsa.+31 Ndipo kwa masiku ambiri anaonekera kwa anthu amene anayenda naye kuchokera ku Galileya kupita ku Yerusalemu. Panopa amenewa ndi mboni zake kwa anthu.+