Aroma 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yesu anaperekedwa chifukwa cha machimo athu+ ndipo anaukitsidwa kuti tionedwe olungama.+ Aheberi 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+
25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+