-
2 Akorinto 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Si zokhazo, koma anasankhidwanso ndi mipingo kuti aziyenda nafe pamene tikupereka mphatso zachifundozi. Tikupereka mphatsozi kuti Ambuye alandire ulemerero komanso kuti tisonyeze kuti tikufunitsitsa kuthandiza ena.
-