Miyambo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzakhala wotetezeka,+Koma munthu wochita zinthu mwachinyengo adzadziwika.+ 2 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa amene amavomerezedwa si wodzikweza,+ koma amene Yehova* wamuvomereza.+ 1 Timoteyo 5:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Machimo a anthu ena amadziwika kwa anthu, ndipo amaweruzidwa nthawi yomweyo. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pakapita nthawi.+ 25 Nazonso ntchito zabwino zimadziwika kwa anthu,+ ndipo zimene sizidziwika sizingabisike mpaka kalekale.+
9 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzakhala wotetezeka,+Koma munthu wochita zinthu mwachinyengo adzadziwika.+
24 Machimo a anthu ena amadziwika kwa anthu, ndipo amaweruzidwa nthawi yomweyo. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pakapita nthawi.+ 25 Nazonso ntchito zabwino zimadziwika kwa anthu,+ ndipo zimene sizidziwika sizingabisike mpaka kalekale.+