Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Malemba amati: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+ 1 Akorinto 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ ngati mmene enanso anachitira,* ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa chifukwa mawa tifa.”+ 2 Akorinto 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+ 2 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati osadziwika koma ndife odziwika bwino, ngati oti tikufa* koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa koma osaperekedwa kuti tikaphedwe,+
32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ ngati mmene enanso anachitira,* ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa chifukwa mawa tifa.”+
4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+
9 ngati osadziwika koma ndife odziwika bwino, ngati oti tikufa* koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa koma osaperekedwa kuti tikaphedwe,+